Ndinanyula – Onesimus

Onesimus wavomereza kuti ananyula usiku wa loweruka pomwe ananyoza amuna. Woyimbayu wati sadzayambiranso ndipo wapempha kuti anthu amukhululukire . Woyimbayu yemwe ena amamuti Chintuwi watulutsa uthenga wake opepesa a Malawi. Loweruka ku mwambo wa zoyimbayimba… ...