Mwini munda anyotsoledwa khutu ndi mlonda
Bambo wa zaka 37 ku Neno akuvutika ndi bala lomwe linadza mlonda wina atamuluma khutu lake pomwe mlondayo ankafuna kulanda munda wa a Walani. Bamboyu Jones Walani akudandaulaso kuti sakudziwa komwe kuli khutu lonyotseledwalo. Bamboyu… ...