Mitengo ya madzi yakwera

Pamene anthu akudandaula kale ndi kukwera kwa mitengo yazinthu zambiri, boma kudzera kuunduna wa zachilengedwe laloleza mabungwe ogulitsa madzi mdziko muno kukweza mitengo. Izi ndimalingana ndi chikalata chomwe undunawu watulutsa posachedwapa chomwe wasainira ndi mlembi… ...