Achinyamata adzikhala ndi mipando ya padera ku nyumba ya Malamulo – Mtumbuka
A Matthews Mtumbuka, omwe alinawo m'gulu lofuna kudzapikisana nawo pa mpando wa utsogoleri kuchipani cha United Transformation (UTM) ati ali ndi malingaliro ofuna kudzayambitsa zoti achinyamata pamodzi ndi amayi azidzakhala ndi mipando yawo yapadera ku… ...