
Muneneze mabanki omwe akukudulani ndalama – Mlusu
Boma kudzera kwa nduna ya zachuma a Felix Mlusu lati anthu omwe akudulidwa ndalama zawo ku mabanki mu dzina la VAT, akanene ku banki ya Reserve kuti ndalama zawo zonse zibwezedwe. A Mlusu amayankhula izi… ...