Chaka chino kuli njala, laopseza motero boma
Boma kudzera ku bungwe losunga chakudya la National Food Reserve Agency (NFRA) lati lili ndi chimanga chochepa mu nkhokwe zake, zomwe zikupeleka chiopsezo kuti njala ivuta chaka chino. Malingana ndi mkulu wa bodi yoyang’anira bungweli… ...