
Ntchito yokonza msika wa Kamba yayambika
Ntchito yokonza msika wa Kamba munzinda wa Blantyre kukhala wa makono (shopping mall), yayambika ndipo pomwe tinathamangira ku malowa lero Lolemba, tinapeza pamalopa pakudulidwa mitengo kusonyeza chiyambi cha ntchitoyi. Mbali inayi, anthu omwe amachita malonda… ...