Mlendo ndimame sachedwa kukamuka: Mneneli Mbewe watuluka PP
Pomwe anthu otsatira chipani cha People's (PP) anali ndi chimwemwe chodzadza tsaya kuti mwina mkutheka Mneneli David Mbewe awatengera mtsidya lina, munthu wa Mulunguyu watuluka mchipanichi atakhalamo maola ochepa. Mneneli Mbewe analowa chipani cha PP… ...