Ma timu ndidziwaphera nzeru osati mphamvu – Joseph Kamwendo
Osewera mpira wa miyendo yemwe ndi m'modzi mwa a chiyamba-kale m’dziko muno, Joseph Kamwendo wati iye akukula koma mu maseweredwe ake a mpira ma timu adziwaphera nzeru. Kamwendo yemwe pakali pano akusewera mpira wake mu… ...