
Ambuye akukanthani nonse onyoza a Chakwera – watero Manganya
A nduna oona za chikhalidwe a Michael Usi amene amadziwikanso ngati Manganya ati Mulungu achita ndi a Malawi onse onyoza a Chakwera. Polankhula pa mwambo okumbukira M'busa John Chilembwe ku Chiradzulu, a Usi anadzudzula a… ...