DPP ikufuna chisankho china

Potsatira kuchotsedwa ntchito kwa makomishonala awiri a bungwe loyendetsa chisankho la MEC, chipani chotsutsa boma cha DPP chati chipita kukhothi kukapempha kuti khothi lilamule kuti chisankho chachibwereza cha chaka chatha chinali chosayenera. Nkhaniyi ikubwera pomwe… ...