Anthu asanu ndi m’modzi anjatidwa pogenda ma ofesi a nthambi yowona zolowa ndi zotuluka
Anthu asanu ndi m’modzi (6) mu nzinda wa Lilongwe, ali m’manja mwa apolisi poganizilidwa kuti anali m'gulu la omwe anagenda ma ofesi a nthambi yowona zolowa ndikutuluka m’dziko muno (DICS) pa nkhani ya ziphaso. Lachinayi… ...