Taimitsa kaye zionetsero – Mtambo
Wapampando wa bungwe lomenyera ufulu wa anthu la Human Rights Defenders Coalition (HRDC) a Timothy Mtambo, alengeza kuti ayamba aimitsa kaye zionetsero pofuna kupereka mpata ku bwalo la milandu lomwe layamba kumva nkhani yokhudza zotsatira… ...