Gwamba

Gwamba asasa mau

Kadaulo pankhani yoyimba nyimbo za uzimu mu chamba cha hip hop Gwamba wanenesa kuti ayimbira Namalenga mpaka kusasa mawu. Gwamba watero mu maimbidwe ake atsopano otchedwa Kusasa Mawu. Nyimboyi yomwe yajambulidwa masabata ochepa apitawo, ikukondedwa… ...