Namadingo alowera ku bibida

Nkhani yomwe inamanga nthenje mu sabata langothali ndiyokhudza katswiri oyimba nyimbo za uzimu Patience Namadingo. Bambo Namadingo ndi amene anayendesa mwambo okhadzikisa chakumwa cha ukali chomwe akufulura a kampani ya Castel, lachisanu lapitali. Ndipo Ku… ...