Boma ligayitsa chimanga chomwe linalanda chochokera ku Tanzania
Ngati njira imodzi yofuna kupewera matenda a chimanga omwe agwa mdziko la Tanzania kuyambukira mdziko muno, boma la Malawi lati likagayitsa chimanga chomwe linalanda anthu ena omwe amafuna achilowetse mdziko muno. Izi zikudza pomwe boma… ...