Nthungululu komanso malikhweru ku Balaka: Escom yakonza vuto la magetsi
Kudamveka kufuula mwa chisangalalo pamene azimai adaimba nthungululu komanso malikhweru adamveka pakati pa abambo ndi achinyamata pamene kampani ya Escom imakonza vuto la magetsi lomwe lidali ku Majiga 2 ntauni ya Balaka. Anthu okhala mdelari… ...