Awiri anjata pofuna kulowetsa chamba ku ndende
Mnyamata wina yemwe amayankha mlandu kale, wamangidwaso kachiwiri pamodzi ndi mzake wina yemwe amafuna kukamupatsira chamba chomwe anachibisa munkhwayira tsiku lakumva mlandu. Malingana ndi ofalitsa nkhani pa Polisi ya Zomba, a Patricia Supuliano, oganizilidwa awiriwa… ...