
Sandram alonjeza kupitiliza kuthandiza chipatala cha South Lunzu
Pali chiyembekezo kuti ntchito pa chipatala cha South Lunzu munzinda wa Blantyre zidziyendako bwino potsatira thandizo la ndalama zokwana K25 miliyoni lomwe Deus Sandram mogwilizana ndi OG Group of Companies komanso Build Africa apereka. Sandram… ...