Mbava zithyola Polisi

Mbava zathyola ndi kuba pa polisi yaying'ono ya Chimbiya m’boma la Dedza. Nkhaniyi ikuti mbavazi zinakaba pa polisiyi nthawi yomwe wapolisi amagwila ntchito yoyang'anila anapita kukakhala nawo pamalo ochitila chipikisheni. Mbavazi zomwe sizikuziwika zinakwanisa kuba… ...