MEC yadula mutu ofuna utsogoleri wa dziko atatu
Bungwe loyendetsa chisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) latchetcha pa mndandanda atsogoleri atatu kuti sakapikisana nawonso pa chisankho chofuna kusankha m'tsogoleri wa dziko lino mwezi wa mawa. Malingana ndi bungweli lero, opikisana khumi ndi asanu… ...