Amunjata chifukwa chonama za ‘anamapopa’
Inu amene mukumadzuka usiku ndi kumakolezera moto pa nkhani zopopa magazi, samalani chifukwa Apolisi ayamba kunjata anthu a mkhalidwe onunkhawu. Mkulu wina wa mu boma la Zomba walamulidwa kukakhala ku ndende kwa miyezi itatu chifukwa… ...