
A Polisi apa msewu anyanya – Christopher Chiomba
Yemwe akufuna kudzapikisana nawo ngati mtsogoleri wa dziko lino pa zisankho zomwe zichitike mwezi wa September pa 16, Christopher Mike Chiomba a chipani cha Nzika Coalition ati ulendo wina anakumana ndi a polisi apa msewu… ...