Tabitha Chawinga awumbuzidwa ndi mphwake
Katswiri okankha chikopa mu timu ya mpira wa miyendo ya fuko lino Tabitha Chawinga adaona ngati kumaloto loweruka lapitali pamene mng'ono wake Temwa Chawinga adamuonesa zakuda. Tabitha adalephera kuithandiza timu yake ya Jiangsu Suning kupeza… ...