M’busa anjatwa, akuti Mulungu anamuuza kuti agwililire
M'busa wina m'boma la Phalombe wa njatwa ndipo wagamulidwa kukaseweza jere zaka khumi ndi mphambu imodzi (11) kaamba kopezeka olakwa pamlandu ogwililira mwana wazaka khumi ndi mphambu zitatu (13). Malingana ndi mneneri wa apolisi m'bomali… ...