Bambo amulamula kukakhala ku ndende zaka 11 chifukwa chogwilirira mwana
Bwalo la milandu ku Liwonde mu boma la Machinga lalamula bambo wina wa zaka 27 zakubadwa kuti akakhale ku ndende ndikukagwila ukaidi wakalavula gaga kwa zaka 11 chifukwa chopezeka olakwa pamulandu ogwirilira mwana wa zaka… ...