Mfumu yayikulu Kumtaja yayipidwa posapatsidwa mpata olankhula pamaso pa a Chakwera
"Ndakwiya kwambiri" yatelo mfumu yayikulu Kumtaja ya m'boma la Blantyre ponena kuti ndi yokhumudwa kwambiri posapatsidwa mpata kuti ilankhure pomwe mafumu a m'bomali amakakumana ndi kucheza ndi m'tsogoleri wa dziko Lazarus Chakwera ku nyumba ya… ...