
Chelsea yakunthidwa
Usiku wa dzulo Brighton yalongosola nsagwada za Chelsea pozipinda katatu pa bwalo la Falmer mu chikho cha English Premier League (EPL) komwe Chelsea inali alendo. Kaoru Mitoma anakhazika chete Chelsea asanabwere Yonkuba Minteh ndi dzilango… ...