
Ndine osalakwa, ndiloleni ndisankhe nawo Papa watsopano- walira mokweza Kadino Becciu
Ma Kadino akulu akulu a mpingo wa katolika, omwe anapatsidwa mphamvu zosankhanso mtsogoleri wa mpingowu, agwidwa kakasi kamba kakuti sanapange chiganizo ngati nkoyenera kuti Kadino yemwe anamangidwapo kamba ka utambwali ozembetsa ndalama aloledwe kulowa mchipinda… ...