
Mutibwenzele ndalama zathu, apo biii tipanga ziwonetsero
Makolo ambiri m'dziko muno ati akufuna bungwe loyendetsa mayeso m'dziko muno la MANEB liwabwenzele ndalama zawo pokhumudwa ndi chiganizo chomwe bungweri lalengeza posachedwapa kuti ophunzira a sitandade 8 alemba mayeso popanda chitupa chowazindikilitsa (ID). Bungweli… ...