Banki yaikulu yakweza chiongola dzanja
Banki yaikulu ya Reserve yalengeza kuti mabanki akwabwereka ndalama tsopano azipereka chiongola dzanja cha K26 pa K100 iliyonse kuchoka pa K24 pa K100 iliyonse. Bankiyi yalengeza izi kutsatira mkumano omwe inachita pa 31 January mpaka… ...