
Ana ongoyendeyenda asumila Ayuba James pa zomwe analemba pa tsamba lake la mchezo
Ana ongoyendeyenda (street kids) asumila m'modzi mwa oyimilira milandu Sylvester Ayuba James pa zomwe analemba pa tsamba lake la mchezo zokhudza anawa. Pa 14 January, 2025, a James analemba pa tsamba lake la mchezo kupempha… ...