Mwana monga bambo: Atupele Muluzi azagawa mafoni 5 million akawina
Yemwe adati dzungu silibala mphonda adalinga ataona. Yemwe ndi mwana wa mtsogoleri wakale wa dziko lino a Bakili Muluzi, Atupele Muluzi wati akazawina azagawa ma lamya a m'manja komaso ma kompyuta kwa maanja zikwi zisanu… ...