Bambo anjatwa chifukwa choluma mlomo wa mwana
A polisi m'boma la Nkhotakota amanga bambo wa zaka 46 chifukwa chomuganizila kuti analuma mlomo wamwana wake wamamuna. Bamboyi, Frankson Chaminju akumuganizila kuti analuma mlomo wamwana wake Chisomo Chaminju wa zaka 18 ati chifukwa chobwela… ...