Malonda athu sakuenda, tikufuna tikambirane ndi a HRDC asiye zionetsero – Leston Mulli
M’modzi mwa anthu amalonda m’dziko muno a Leston Mulli ati ndiokhudzidwa kaamba kakusokonekela kwa ntchito za malonda chifukwa cha zionetsero m’dziko muno ndipo akambirana ndi a mabungwe kuti asiye zionetsero. A Mulli amalankhula izi pansonkhano… ...