Zamasiku omaliza: Munthu azitchula kuti ndi mulungu
Pomwe bukhu lopatulika limafotokoza bwino zomwe zizachitike masiku omaliza, bambo wina akuzitcha kuti iye ndi mulungu ndipo anthu a mumpingo mwake akumamulambira. Bamboyu yemwe dzina lake ndi Overtone Makuta wati iyeyo ndi mulungu kotero kuti… ...