
113 million Kwacha pa masewelo a Silver ndi Bullets
Bwalo la Bingu mu mzinda wa Lilongwe lero lakwanitsa kutulutsa ndalama za nkhani-nkhani zokwana 113 million Kwacha kuchokera mu masewelo amodzi a Silver Strikers ndi FCB Nyasa Big Bullets. Masewelowa omwe anali otsekulira season ya… ...