
A President, mukhiyeni Chaponda – atero anthu a DPP
Zafika pano mzawo wa a Chaponda atha kukhala a Peter Mutharika okha ndi oyimba uja Joseph Nkasa. Anthu otsatila chipani cholamula cha Democratic Progressive (DPP) apempha mtsogoleri wa dziko lino amenenso ndi mtogoleri wawo a… ...