MEC yapempha kudekha, bata panthawi yachisankho
...50+1 ndiyomwe igwiritsidwe ntchito.... Bungwe loyendetsa zisankho m’dziko muno la Malawi Electoral Commission (MEC) lapempha anthu kuti akhale odekha komanso asunge bata ndi mtendere pomwe dziko lino likhale likuchita chisankho cha mtsogoleri wadziko lachiwiri lino.… ...