Armyworms

Ntchembere zandonda zagwa

Unduna wa ulimi, ulimi wa nthirira ndi chitukuko chamadzi wati ntchembere zandonda zikuonononga mbewu zosiyanasiya m’madera ambiri m’dziko muno. Mbozizi zagwa chifukwa chakusintha Kwa nyengo m’madea ambiri mdziko muno. Izi zili chomwechi potsatira mvula yankutho… ...