Chakwera akutsekulira nsika wa fodya
Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera, lero ali m’boma la Kasungu komwe watsegulira nyumba ya Tobacco Commission yomwe yamangidwa posachedwapa komanso akuyembekezeka kutsekulira nsika wa fodya ndi kuyendera nyumba za asilikali zomwe zikumangidwa. Izi ndi… ...