The Democratic Progressive Party (DPP) says Member of Parliament for Mwanza Central Nicholas Dausi is no longer a member of the party. DPP spokesperson Shadric Namalomba has said this in a statement today. According to… ...
Dambwe laotchedwa
Asilamuwo atentha dambwe m'mudzi wa Mchinga kwa mfumu Njombwa ku Kasungu chifukwa gule wamkulu anagwira mwana wa mtsogoleri wachisilamu kukalowa naye ku dambweko. Malingana ndi wailesi ya Zodiak, gule wamkulu anagwira mwana wa mtsogoleri wachisilamu… ...
Bon Kalindo
Malawi Police have arrested activist Bon Kalindo over his attempt to go ahead with demonstrations which are aimed at demanding President Lazarus Chakwera to step down. Kalindo was at Lilongwe District Council offices today following… ...
Partner of a police officer in Malawi
Wapolisi ku Thyolo wamwa magalasi pofuna kuzipha chifukwa choti anatentha mkazi wake ndi madzi owotcha. Wapolisiyi dzina lake ndi Constable Elson Mnyalira ndipo amagwira ku PMS G Division ku Thyolo. Mneneri wa apolisi mchigawo cha… ...