Malawi Police Service (MPS)
Apolisi ati chiwelengero cha amuna amene akudzipha okha m'dziko muno chikukwera kwambiri. Malingana ndi lipoti limene atulutsa akulikulu la apolisi ku Lilongwe, amuna okwana 246 achotsa miyoyo yawo kuyambira mu mwezi wa January kufika June… ...