Edgar Kulemeka
Bambo Edgar Kulemeka amene pa 11 mwezi uno anabaya Mayi Sally Mkwezalamba pofuna kuthawa ngongole anjatidwa tsopano. Malinga ndi Apolisi, achibale a Kulemeka ndiwo anakatula mkuluyo ku Polisi patatha sabata akuyenda chothawathawa. A Kulemeka ati… ...
Mcp supporters
Kunali kanthu ku Balaka pamene chipani chotsutsa cha Kongeresi chinachititsa msonkhano pa sukulu ya Balaka Primary. Msonkhanowu umene unasonkhanitsa akuluakulu a chipanichi kuphatikizapo a Sidik Mia unakodola khamu loti a Kongeresi sanalionepo ku chigawo cha… ...