Carlsberg Cup
Awatibulanso. Kachikena awatsambitsa madzi a matope. Ku Bingu anapita akusangalala kuja, Manoma atuluka ndi nkhope zozyolika akulila mayomayo. Pa masewero amene anakodola khamu, maule lero aliritsa nyerere kachikena atazitsomphola chikho cha Carlsberg. Anali masewero oyamba… ...
Uladi Mussa
...JB has no mandate over PP, says Uladi Mussa Things have fallen apart in People's Party where Uladi Mussa, the party's acting president, has said he no longer recognises Joyce Banda as PP's president. Change… ...
A Roman Catholic priest serving Balaka Parish was found dead on Wednesday. According to the Catholic Secretariat of the Episcopal Conference of Malawi (ECM), Reverend Father Callisto Baluwa of the Society of Montfort Missionaries was… ...
Be Foward Wanderers
Mapeto a sabata awa anali okoma kwambiri kwa nyerere. Atagonjetsa timu ya Moyale pachiwelu, dzulo anaswanso khofi kwa ana asukulu a Mzuni pakwawo pomwe. Pa masewero amene anachitika pa Mzuzu stadium a mpikisano wa ligi,… ...