Over 7200 residents in some parts of Nkhata-Bay lack access to local radio stations as there have been no local radio signal in the areas for decades. Community members in Thotho, Mangw'ina, Musinjiyiwi, Chisangawe, Masasa,… ...
Articles By Ephraim Mkali Banda
Anthu okwana pafupifupi 7,200 okhala m'madera ena akumidzi m'boma la Nkhata-Bay alibe mwayi opeza mauthenga osiyanasiyana kudzera pa wailesi popeza mawayilesi samveka kumaderawa kuyambira nthawi ya atsamunda. Madera monga Thotho, Mangw'ina, Musinjiyiwi, Chisangawe, Masasa, Chitundu… ...
The Malawi Immigration Department says it is currently unable to issue passports due to technical challenges. The department had said this in a0ppp0ppppp0p00 statement to the Malawians. "We are informing Malawians that our passport printing… ...
Mavuta akuwoneka kuti sakutha ku nthambi yowona za anthu olowa ndi kutuluka m'dziko muno (immigration) pomwe nthambiyi yati ikukanika kutulutsa ziphaso zoyendera (Passport). Izi ndi malingana ndi uthenga wa nthambiyi kupita kwa a Malawi wati.… ...
Communities living around Mtende Health Centre in Mzimba District have asked health officials to transfer in-charge of the facility who is answering a case of harming his 5-year-old son by burning his finger with charcoal… ...
Mfumu Chawola ya dera la Kangoi yomwe ili pansi pa Mfumu ya yikulu Timbiri M'boma la Nkhata Bay yati iyo limodzi ndi anthu awo ndiwokondwa kuti tsopano ntchito za umoyo pa chipatala chaching'ono cha Kangoi… ...
Khoti la Euthini, m'boma la Mzimba lagamula Martha Chaula wa zaka 47, kukakhala kundende kwa miyezi 18 popezeka wolakwa pa mulandu wofuna kuba khanda. Bwaloli linamva kuti mayiyu anachita izi pofuna kusangalatsa mamuna wake, yemwe… ...