Rights group, Centre for Democracy and Economic Development Initiatives (CDEDI), has demanded the Malawi government to reverse its decision to construct a MK9.4 billion swimming pool. In a press statement, CDEDI Executive Director Sylvester Namiwa… ...
A kunyumba ya boma atsutsa mphekesera zoti mu mgwirizano wa Tonse muli mpungwepungwe. Nkhaniyi ikutsatira manong'onong'o omwe akhala akumveka makamaka pamasamba amchezo oti akuluakulu azipani zomwe zili mugwirizanowu sakumwerana madzi kaamba kosepmhana chichewa pazinthu zina.… ...
Twenty-year-old George Kalichelo from Mulanje who built an electricity-generating windmill using scraps and created a semi-electric mbaula (cook stove), is seeking support to enhance his talent. Kalichero from Duswa village in the area of Traditional Authority… ...
Limodzi mwa mabungwe omenyera ufulu mdziko muno la Center for Human Rights and Rehabilitation (CHRR) lati a Ken Kandodo omwe anali nduna ya za ntchito akuyenera amangidwe pankhani yakusakazidwa kwa ndalama za mlili wa covid-19.… ...