Mtsogoleri wa mpingo wa Enlightened Christian Gathering (ECG) Shepherd Bushiri wati ayamba kuthandiza mwana yemwe posachedwapa anaonesedwa m’masamba a nchezo akudyetsedwa dowe wa muwisi. Posachedwapa, anthu ambiri m’masamba a nchezo anagwidwa ndi chisoni kamba ka… ...