“Osewera tagwirizana kutenga zikho zonse,” mhuuu! Anakadziwa sanakayankhula, maloto a chumba enieni, chimanjamanja ikutuluka m'chakachi. Tsoka la mfutso lopita pa moto kawiri ndipo kupsa kwake ndi kwa chigumu, pansi ndi pa mwamba. Mukutipheranji? Walira movetsa… ...
Anthu akudera la mfumu yaikulu Mtumbwinda m’boma la Machinga, akukhala mwa mantha kamba ka afisi olusa omwe akuti kumayambiliro a mwezi uno apha munthu m’modzi komaso loweluka lapitali avulazaso munthu wina. Yatsimikiza za nkhaniyi ndi… ...