Hastings Salanje Malawian Pastor
Akuluakulu a mpingo wa God's Chapel alengeza kuti zigawenga zomwe zinasowetsa mtsogoleri wawo Hastings Salanje masiku angapo apitawa, zamulavura tsopano ndipo ali bwino bwino. Pa 1 December chaka chino, akuluakulu a mpingo wa God's Chapel… ...
Malawi President Peter Mutharika and Kondwani Nankhumwa
Kuli kanthu kokanthula nchala mchipani cha Democratic Progressive (DPP) pomwe mtsogoleri wake a Peter Mutharika achotsa a Kondwani Nankhumwa pa udindo wa wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipanichi mchigawo chakum'mwera. Izi ndimalinga ndi kalata yomwe chipani… ...